Ekisodo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndipatulireni mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa ana a Isiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+ Luka 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Izi zinali zogwirizana ndi zimene Malemba amanena m’chilamulo cha Yehova kuti: “Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa adzakhala woyera kwa Yehova.”*+
2 “Ndipatulireni mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa ana a Isiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+
23 Izi zinali zogwirizana ndi zimene Malemba amanena m’chilamulo cha Yehova kuti: “Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa adzakhala woyera kwa Yehova.”*+