Ekisodo 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zimene uzichita ndi mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe ndi wa nkhosa yako ndi izi:+ Azikhala ndi mayi wake masiku 7.+ Pa tsiku la 8 uzim’pereka kwa ine.
30 Zimene uzichita ndi mwana woyamba kubadwa wa ng’ombe ndi wa nkhosa yako ndi izi:+ Azikhala ndi mayi wake masiku 7.+ Pa tsiku la 8 uzim’pereka kwa ine.