Ekisodo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Mose anatenga magaziwo ndi kuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndiwo magazi okhazikitsira pangano+ limene Yehova wapangana nanu mwa mawu onsewa.” Deuteronomo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+
8 Pamenepo Mose anatenga magaziwo ndi kuwaza anthuwo,+ ndipo anati: “Awa ndiwo magazi okhazikitsira pangano+ limene Yehova wapangana nanu mwa mawu onsewa.”
13 Pamenepo anakuuzani pangano lake,+ Mawu Khumi,*+ ndipo anakulamulani kuti muzilisunga. Kenako analemba Mawu Khumiwo pamiyala iwiri yosema.+