Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 31:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+

  • Deuteronomo 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamiyalayo ndidzalembapo mawu amene anali pamiyala yoyamba ija, imene unaswa, ndipo udzaiike m’likasalo.’

  • 2 Akorinto 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 ndipo chifukwa cha iyeyo ndife oyenera kukhala atumiki a pangano latsopano,+ ndipo ndife ogwirizana osati kudzera m’malamulo olembedwa,+ koma mu mzimu.+ Pakuti malamulo olembedwa amaweruza munthu+ kuti afe, koma mzimu umapatsa munthu moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena