Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako, Mose anatembenuka n’kutsika m’phirimo+ atanyamula miyala yosema ya Umboni+ m’manja mwake. Miyalayo inali yolembedwapo mawu mbali zonse ziwiri. Inali yolembedwapo mawu mbali iyi ndi mbali inayo.

  • 2 Akorinto 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti zikuonekeratu kuti ndinu kalata yochokera kwa Khristu yolembedwa ndi ifeyo kudzera mu utumiki wathu.+ Kalatayo siyolembedwa ndi inki koma ndi mzimu+ wa Mulungu wamoyo. Siyolembedwa pazolembapo zamiyala,+ koma zamnofu, pamitima.+

  • Aheberi 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mmenemu munali chiwaya chagolide chofukizira nsembe,+ ndi likasa la pangano.+ Likasa lonseli linali lokutidwa ndi golide.+ M’likasamo munali mtsuko wagolide wokhala ndi mana.+ Munalinso ndodo ya Aroni imene inaphuka ija,+ komanso miyala yosema+ ya pangano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena