Ekisodo 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ulumikize nsalu zisanu pazokha, kenako ulumikizenso nsalu 6 pazokha,+ ndipo upinde pakati nsalu ya 6 ya koyambirira kwa nsalu zolumikizanazo.
9 Ulumikize nsalu zisanu pazokha, kenako ulumikizenso nsalu 6 pazokha,+ ndipo upinde pakati nsalu ya 6 ya koyambirira kwa nsalu zolumikizanazo.