Ekisodo 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga+ khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ya ulusi wofiira kwambiri, ndi ya ulusi wopota wabwino kwambiri.
36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga+ khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ya ulusi wofiira kwambiri, ndi ya ulusi wopota wabwino kwambiri.