Ekisodo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Upangenso mitengo yonyamulira ya mtengo wa mthethe ndi kuikuta ndi golide.+ 2 Mbiri 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mitengo yonyamulirayo inali yaitali, moti nsonga zake zinali kuonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinali kuoneka kunja. Mitengo yonyamulirayo ikadali pomwepo mpaka lero.+
9 Koma mitengo yonyamulirayo inali yaitali, moti nsonga zake zinali kuonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinali kuoneka kunja. Mitengo yonyamulirayo ikadali pomwepo mpaka lero.+