Ekisodo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kumbali ziwiri za guwalo upangeko mphete zagolide, ziwiri kumbali iyi ndi zinanso ziwiri kumbali inayo. Uzipange m’munsi mwa mkombero kuti muzilowa mitengo yonyamulira guwalo.+
4 Kumbali ziwiri za guwalo upangeko mphete zagolide, ziwiri kumbali iyi ndi zinanso ziwiri kumbali inayo. Uzipange m’munsi mwa mkombero kuti muzilowa mitengo yonyamulira guwalo.+