Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 30:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakaniza mwaluso.+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.+

  • Ekisodo 30:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Aliyense wopanga mafuta ofanana ndi amenewa, ndiponso amene angapake munthu wamba, ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.’”+

  • Ekisodo 40:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno udzatenge mafuta odzozera+ ndi kudzoza chihema chopatulika ndi zonse zimene zili mkati mwake.+ Motero udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika.

  • 1 Mbiri 9:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ena mwa ana a ansembe anali opanga mafuta onunkhira+ osakaniza ndi mafuta a basamu.

  • Salimo 45:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+

      N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+

  • Aheberi 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Unakonda chilungamo ndipo unadana ndi kusamvera malamulo. N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako, anakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu kuposa cha mafumu ena.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena