Ekisodo 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso mulandire miyala ya onekisi ndi miyala yozika pa efodi*+ ndi pachovala pachifuwa.+ Levitiko 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anamuveka chovala cha pachifuwa+ ndi kuika Urimu ndi Tumimu+ m’chovala cha pachifuwacho.