Ekisodo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.* Ekisodo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano m’masiku amenewo pamene Mose anali kukula ndi kukhala wamphamvu, anapita kwa abale ake kuti akaone ntchito imene anali kugwira.+ Kumeneko anaona m’bale wake wachiheberi akumenyedwa ndi Mwiguputo.+
11 Choncho anawaikira akulu owayang’anira pa ntchito yawo yaukapolo, kuti aziwanyamulitsa katundu mwankhanza.+ Ndipo anamangira Farao mizinda ya Pitomu ndi Ramese+ kuti ikhale mosungiramo zinthu.*
11 Tsopano m’masiku amenewo pamene Mose anali kukula ndi kukhala wamphamvu, anapita kwa abale ake kuti akaone ntchito imene anali kugwira.+ Kumeneko anaona m’bale wake wachiheberi akumenyedwa ndi Mwiguputo.+