Ekisodo 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atatero anapanga ngowe 50 zamkuwa zolumikizira nsaluzo kuti zikhale chinsalu chimodzi.+