Ekisodo 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno anapanga chophimba chihemacho cha zikopa za nkhosa zonyika mu utoto wofiira, ndi chophimba chinanso cha pamwamba pake cha chikopa cha akatumbu.+
19 Ndiyeno anapanga chophimba chihemacho cha zikopa za nkhosa zonyika mu utoto wofiira, ndi chophimba chinanso cha pamwamba pake cha chikopa cha akatumbu.+