Ekisodo 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero anapanga ziwiya za patebulolo, mbale zake, zikho zake, mitsuko yake ndi mbale zake zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Anazipanga ndi golide woyenga bwino.+
16 Atatero anapanga ziwiya za patebulolo, mbale zake, zikho zake, mitsuko yake ndi mbale zake zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Anazipanga ndi golide woyenga bwino.+