-
Ekisodo 38:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Ndipo mkuwa umenewu anaugwiritsa ntchito kupangira zitsulo zamphako zokhazikapo mizati ya pakhomo la chihema chokumanako, guwa lansembe lamkuwa, sefa wa guwalo wa zitsulo zolukanalukana ndi ziwiya zonse zogwiritsa ntchito paguwalo.
-