Ekisodo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo iwe ulankhule ndi anthu onse aluso amene ndinadzaza mzimu wa nzeru+ m’mitima yawo kuti amupangire Aroni zovala zomuyeretsa, kuti atumikire monga wansembe wanga.+
3 Ndipo iwe ulankhule ndi anthu onse aluso amene ndinadzaza mzimu wa nzeru+ m’mitima yawo kuti amupangire Aroni zovala zomuyeretsa, kuti atumikire monga wansembe wanga.+