Numeri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema chopatulika,+ anachidzoza+ n’kuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, komanso guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse. Zonse anazidzoza n’kuzipatula.+
7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema chopatulika,+ anachidzoza+ n’kuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, komanso guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse. Zonse anazidzoza n’kuzipatula.+