Ekisodo 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga+ khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ya ulusi wofiira kwambiri, ndi ya ulusi wopota wabwino kwambiri. Ekisodo 39:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 guwa lansembe+ lagolide, mafuta odzozera,+ zofukiza zonunkhira,+ nsalu yotchinga+ pakhomo la chihemacho,
36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga+ khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ya ulusi wofiira kwambiri, ndi ya ulusi wopota wabwino kwambiri.
38 guwa lansembe+ lagolide, mafuta odzozera,+ zofukiza zonunkhira,+ nsalu yotchinga+ pakhomo la chihemacho,