2 Mafumu 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe wanena kuti (koma ndi mawu a pakamwa chabe), ‘Ine ndili ndi nzeru+ ndi mphamvu zofunika pankhondo.’ Kodi ukudalira ndani popandukira+ ine? Yeremiya 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Azariya mwana wa Hoshaya,+ Yohanani+ mwana wa Kareya ndi anthu enanso odzikuza+ anauza Yeremiya kuti: “Ukunena zabodza. Yehova Mulungu wathu sanakutume kudzatiuza+ kuti, ‘Musapite ku Iguputo kuti mukakhale kumeneko monga alendo.’+
20 Iwe wanena kuti (koma ndi mawu a pakamwa chabe), ‘Ine ndili ndi nzeru+ ndi mphamvu zofunika pankhondo.’ Kodi ukudalira ndani popandukira+ ine?
2 Azariya mwana wa Hoshaya,+ Yohanani+ mwana wa Kareya ndi anthu enanso odzikuza+ anauza Yeremiya kuti: “Ukunena zabodza. Yehova Mulungu wathu sanakutume kudzatiuza+ kuti, ‘Musapite ku Iguputo kuti mukakhale kumeneko monga alendo.’+