Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 8:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Atatero Mose anatengako mafuta odzozera+ ndi magazi amene anali paguwa lansembe aja n’kuwawaza pa Aroni ndi pazovala zake. Anawawazanso pa ana ake aja ndi pazovala zawo. Motero anapatula+ Aroni ndi zovala zake komanso ana a Aroni+ ndi zovala zawo.

  • 2 Akorinto 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma amene amatitsimikizira kuti inuyo ndi ife tili a Khristu, amenenso anatidzoza,+ ndiye Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena