Aheberi 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+ Aheberi 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero abale, ndife olimba mtima chifukwa tikugwiritsa ntchito njira yolowera+ m’malo oyera+ kudzera m’magazi a Yesu.
3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+
19 Chotero abale, ndife olimba mtima chifukwa tikugwiritsa ntchito njira yolowera+ m’malo oyera+ kudzera m’magazi a Yesu.