Ekisodo 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo patebulopo uziikapo mkate wachionetsero pamaso panga nthawi zonse.+ Mateyu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+
4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+