Ekisodo 25:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndipo uchipangire nyale 7. Nyalezo ziziyatsidwa kuti ziziunikira patsogolo pake.+ Ekisodo 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno anachipangira nyale 7, zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+ Salimo 119:105 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,+Ndi kuwala kounikira njira yanga.+
23 Ndiyeno anachipangira nyale 7, zopanira zake zozimitsira nyale ndi mbale zake zoikamo phulusa la zingwe za nyale. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+