Ekisodo 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Aroni azifukiza zofukiza zonunkhira paguwapo.+ M’mawa uliwonse akamasamalira nyale,+ azifukiza zofukizazo. Ekisodo 30:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zinthu zimenezi upangire zofukiza,+ msanganizo wa zonunkhiritsa zosakaniza mwaluso, wothira mchere,+ msanganizo weniweni wopatulika.
7 “Aroni azifukiza zofukiza zonunkhira paguwapo.+ M’mawa uliwonse akamasamalira nyale,+ azifukiza zofukizazo.
35 Zinthu zimenezi upangire zofukiza,+ msanganizo wa zonunkhiritsa zosakaniza mwaluso, wothira mchere,+ msanganizo weniweni wopatulika.