Ekisodo 38:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno anapanga guwa lansembe zopsereza la matabwa a mthethe, m’litali mwake mikono isanu, ndipo m’lifupi mikono isanu. Guwalo linali lofanana muyezo wake mbali zake zonse zinayi, ndipo msinkhu wake linali mikono itatu.+ Aheberi 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ife tili ndi guwa lansembe limene ochita utumiki wopatulika kuchihema, alibe ulamuliro wodya za paguwapo.+
38 Ndiyeno anapanga guwa lansembe zopsereza la matabwa a mthethe, m’litali mwake mikono isanu, ndipo m’lifupi mikono isanu. Guwalo linali lofanana muyezo wake mbali zake zonse zinayi, ndipo msinkhu wake linali mikono itatu.+
10 Ife tili ndi guwa lansembe limene ochita utumiki wopatulika kuchihema, alibe ulamuliro wodya za paguwapo.+