Ekisodo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Anthu amenewa musawapezerenso udzu woumbira njerwa+ ngati kale. Muwasiye azikafuna okha udzu umenewo.
7 “Anthu amenewa musawapezerenso udzu woumbira njerwa+ ngati kale. Muwasiye azikafuna okha udzu umenewo.