Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo anasautsa moyo wa Aisiraeliwo powagwiritsa ntchito yowawa yaukapolo, yomwe inali yoponda matope+ ndi kuumba njerwa.* Anawagwiritsa ntchito yaukapolo wa mtundu uliwonse m’munda,+ ndi ukapolo wa mtundu uliwonse umene anatha kuwagwiritsa ntchito mwankhanza.+

  • Ekisodo 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+

  • Ekisodo 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+

  • Aroma 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti ponena za Farao, Lemba linati: “Ndakusiya ndi moyo kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena