Ekisodo 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atakumana, Mose anauza Aroni mawu onse a Yehova, yemwe anam’tuma.+ Anamuuzanso zizindikiro zonse zimene anam’lamula kuchita.+
28 Atakumana, Mose anauza Aroni mawu onse a Yehova, yemwe anam’tuma.+ Anamuuzanso zizindikiro zonse zimene anam’lamula kuchita.+