Ekisodo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova analola Farao kuumitsabe mtima wake,+ ndipo sanalole ana a Isiraeli kuchoka.