Ekisodo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe ngati sakakhulupirira zizindikiro ziwirizi ndi kumvera mawu ako,+ ukatenge madzi a mumtsinje wa Nailo n’kuwathira panthaka youma. Ndipo madziwo, amene ukatenge mumtsinje wa Nailo, adzasanduka magazi panthakapo. Ndithu adzasanduka magazi.”+
9 Komabe ngati sakakhulupirira zizindikiro ziwirizi ndi kumvera mawu ako,+ ukatenge madzi a mumtsinje wa Nailo n’kuwathira panthaka youma. Ndipo madziwo, amene ukatenge mumtsinje wa Nailo, adzasanduka magazi panthakapo. Ndithu adzasanduka magazi.”+