Ekisodo 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Yenda kutsogolo kwa anthu+ ndipo utenge ena mwa akulu a Isiraeli komanso ndodo yako imene unamenya nayo mtsinje wa Nailo.+ Uitenge m’dzanja lako ndipo uziyenda.
5 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Yenda kutsogolo kwa anthu+ ndipo utenge ena mwa akulu a Isiraeli komanso ndodo yako imene unamenya nayo mtsinje wa Nailo.+ Uitenge m’dzanja lako ndipo uziyenda.