Ekisodo 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo ndidzaika malire pakati pa anthu anga ndi anthu ako.+ Mawa chizindikiro chimenechi chidzachitika.”’” Salimo 76:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu adzatsitsa atsogoleri odzikuza.+Iye ndi wochititsa mantha kwa mafumu a padziko lapansi.+
23 Ndipo ndidzaika malire pakati pa anthu anga ndi anthu ako.+ Mawa chizindikiro chimenechi chidzachitika.”’”