Ekisodo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kumeneko ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wandituma kwa iwe+ ndi uthenga wonena kuti: “Lola anthu anga kuchoka kuti akanditumikire m’chipululu,”+ koma kufikira tsopano sukundimvera.
16 Kumeneko ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wandituma kwa iwe+ ndi uthenga wonena kuti: “Lola anthu anga kuchoka kuti akanditumikire m’chipululu,”+ koma kufikira tsopano sukundimvera.