Ekisodo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzatambasula dzanja langa+ ndi kukantha Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzazichita m’dzikolo. Pamenepo adzakulolani kuchoka.+ Ekisodo 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 dziwa kuti, dzanja la Yehova+ lipha ziweto zanu zonse.+ Mliri waukulu kwambiri ugwera mahatchi,* abulu, ngamila, ng’ombe ndi nkhosa.+
20 Ndidzatambasula dzanja langa+ ndi kukantha Iguputo ndi ntchito zanga zonse zodabwitsa zimene ndidzazichita m’dzikolo. Pamenepo adzakulolani kuchoka.+
3 dziwa kuti, dzanja la Yehova+ lipha ziweto zanu zonse.+ Mliri waukulu kwambiri ugwera mahatchi,* abulu, ngamila, ng’ombe ndi nkhosa.+