Salimo 105:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anawononga mitengo yawo ya mpesa ndi ya mkuyu,Ndipo anakhadzula mitengo m’dziko lawo.+