Ekisodo 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Farao anauza Mose kuti: “Choka!+ Samala! Ndisadzakuonenso, chifukwa ndikadzangokuonanso udzafa.”+
28 Choncho Farao anauza Mose kuti: “Choka!+ Samala! Ndisadzakuonenso, chifukwa ndikadzangokuonanso udzafa.”+