Salimo 105:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Dzombelo linadya zomera zonse m’dziko lawo.+Linadyanso mbewu zonse za m’munda mwawo.