Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Ukadzatero adzamvera mawu ako.+ Pamenepo, iweyo ndi akulu a Isiraeli mudzapite kwa mfumu ya Iguputo ndi kuiuza kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi+ walankhula nafe.+ Chotero mutilole chonde, tiyende ulendo wamasiku atatu m’chipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wathu.’+

  • Ekisodo 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma iwo anati: “Mulungu wa Aheberi walankhula nafe.+ Chotero mutilole chonde, tipite ulendo wamasiku atatu m’chipululu, kuti tikapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wathu.+ Ngati sititero, adzatipha ndi mliri kapena lupanga.”+

  • Ekisodo 8:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ife tidzapita ulendo wamasiku atatu m’chipululu, ndipo kumeneko tikapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wathu, monga momwe watiuzira.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena