Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mkazi aliyense adzapemphe zinthu zasiliva, zagolide, ndi zovala kwa munthu wokhala naye pafupi ndi kwa mlendo wamkazi wokhala m’nyumba mwake. Zinthu zimenezi mudzaveke ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mudzatenge zinthu zambiri za Aiguputo.”+

  • Ekisodo 12:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+

  • Salimo 105:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndiyeno anayamba kuwatulutsa atatenga siliva ndi golide.+

      Pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira.

  • Miyambo 13:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena