Ekisodo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero ndidzachititsa Aiguputo kukomera mtima anthu anga, moti pochoka simudzachoka chimanjamanja.+ Ekisodo 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho Yehova anachititsa Aiguputo kukomera mtima anthu ake,+ moti Aiguputo anawapatsa zinthu zonse zimene anapempha,+ ndipo iwo anatenga zinthu zambiri za Aiguputo.+
21 Chotero ndidzachititsa Aiguputo kukomera mtima anthu anga, moti pochoka simudzachoka chimanjamanja.+
36 Choncho Yehova anachititsa Aiguputo kukomera mtima anthu ake,+ moti Aiguputo anawapatsa zinthu zonse zimene anapempha,+ ndipo iwo anatenga zinthu zambiri za Aiguputo.+