Ekisodo 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zitatero Farao, atumiki ake onse ndi Aiguputo onse anadzuka pakati pa usiku. Ndipo anthu anayamba kulira kwambiri m’dziko lonse la Iguputo,+ chifukwa panalibe banja ngakhale limodzi limene linalibe maliro.
30 Zitatero Farao, atumiki ake onse ndi Aiguputo onse anadzuka pakati pa usiku. Ndipo anthu anayamba kulira kwambiri m’dziko lonse la Iguputo,+ chifukwa panalibe banja ngakhale limodzi limene linalibe maliro.