Deuteronomo 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Uziiwotcha ndi kuidya+ pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe,+ ndipo m’mawa mwake uzitembenuka ndi kubwerera kumahema ako. Mateyu 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ ophunzira anabwera kwa Yesu ndi kumufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako pasika?”+
7 Uziiwotcha ndi kuidya+ pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe,+ ndipo m’mawa mwake uzitembenuka ndi kubwerera kumahema ako.
17 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ ophunzira anabwera kwa Yesu ndi kumufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako pasika?”+