Mateyu 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi ina, Yesu anali kudutsa m’munda wa tirigu pa tsiku la sabata.+ Ophunzira ake anamva njala ndipo anayamba kubudula ngala za tirigu n’kumadya.+
12 Pa nthawi ina, Yesu anali kudutsa m’munda wa tirigu pa tsiku la sabata.+ Ophunzira ake anamva njala ndipo anayamba kubudula ngala za tirigu n’kumadya.+