Aheberi 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwa chikhulupiriro, iye anachita pasika+ ndiponso anawaza magazi pamafelemu a pakhomo,+ kuti wowonongayo asakhudze ana awo oyamba kubadwa.+
28 Mwa chikhulupiriro, iye anachita pasika+ ndiponso anawaza magazi pamafelemu a pakhomo,+ kuti wowonongayo asakhudze ana awo oyamba kubadwa.+