Ekisodo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Tsopano uona zimene ndichite kwa Farao.+ Chifukwa cha dzanja lamphamvu, iye awalola kuchoka, ndipo chifukwa cha dzanja lamphamvu awatulutsa m’dziko lake.”+ Yuda 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+
6 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Tsopano uona zimene ndichite kwa Farao.+ Chifukwa cha dzanja lamphamvu, iye awalola kuchoka, ndipo chifukwa cha dzanja lamphamvu awatulutsa m’dziko lake.”+
5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+