Numeri 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atanyamuka ku Sukoti anakamanga msasa ku Etamu,+ pafupi ndi chipululu.