Salimo 105:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mulungu anayala mtambo kuti uziwatchinga,+Ndipo anawapatsa moto kuti uziwaunikira usiku.+ 1 Akorinto 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano sindikufuna kuti mukhale osadziwa abale, kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+
10 Tsopano sindikufuna kuti mukhale osadziwa abale, kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+