Deuteronomo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Kuwonjezera apo, pa Tabera,+ pa Masa+ ndi pa Kibiroti-hatava+ munaputanso mkwiyo wa Yehova.+ Deuteronomo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+
8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+