Yoswa 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Monga Yehova analamulira mtumiki wake Mose, nayenso Mose analamula Yoswa,+ ndipo Yoswayo anachitadi zimenezo. Palibe mawu alionse amene Yoswa anasiya pa mawu onse amene Yehova analamula Mose.+
15 Monga Yehova analamulira mtumiki wake Mose, nayenso Mose analamula Yoswa,+ ndipo Yoswayo anachitadi zimenezo. Palibe mawu alionse amene Yoswa anasiya pa mawu onse amene Yehova analamula Mose.+